Achenjeza maboma 23 za nyengo ya el nino
Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya DoDMA yachenjeza kuti ulosi woyamba wa nyengo ya mvula ya chaka chino wasonyeza kuti maboma 23 mwa maboma 28 m’dziko muno adzakhudzidwa ndi ng’amba yobwera ndi mphepo ya El-Nino. Ena mwa maboma omwe akuyembekezeka kudzakhudzidwa ndi a Balaka, Blantyre, Blantyre City, Chikwawa, Chiradzulu, Dedza, Dowa, Kasungu, Lilongwe City, … The post Achenjeza m
See all — Malawi Nation →Aggregated from the leading newsrooms of the country. Every story links to its original source.







