‘Lamya zikadathandiza kafukufuku wa ndege’
Lamya za m’manja za omwe adali m’ndege ya asilikali a nkhondo yomwe idagwera ku Chikangawa zikadapezeka msanga n’kuchitidwa chipikisheni zidakatha kuthandiza kupeza chilungamo cha ngoziyo. Umu ndimo katswiri wodziwa zamafoni ndi chipikisheni pogwiritsa ntchito makina a makono a Kingsley Goliati adafotokozera komiti yapadera ya ku Nyumba ya Malamulo yomwe ikufufuza za ngoziyo Lachiwiri. Nyumba ya &
See all — Malawi Nation →Aggregated from the leading newsrooms of the country. Every story links to its original source.







